Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 3/09 tsamba 4
  • Ndandanda ya Mlungu wa April 6

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa April 6
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2009
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA APRIL 6
Utumiki Wathu wa Ufumu—2009
km 3/09 tsamba 4

Ndandanda ya Mlungu wa April 6

MLUNGU WOYAMBIRA APRIL 6

Nyimbo Na. 37

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

cl-CN mutu 17, ndime 9-14

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Eksodo 7-10

Na. 1: Eksodo 9:1-19

Na. 2: Amene Anakhala Ophunzira a Yesu (lr-CN mutu 13)

Na. 3: Kodi Agalatiya 6:2 ndi Agalatiya 6:5 Amatanthauza Chiyani?

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 52

Mph. 5: Zilengezo.

Mph. 10: Mmene Tingaperekere Zifukwa Zomveka. Nkhani ndi kukambirana ndi omvera, yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, masamba 255-257.

Mph. 20: Achinyamata—Kodi Moyo Wanu Mudzaugwiritsa Ntchito Bwanji? Mkulu akambirane ndi omvera kapepala kakuti Moyo Wanu. Ayamikireni ndi mtima wonse achinyamata obatizidwa amene akuika zinthu za Ufumu patsogolo. Funsani mwachidule mmodzi amene anayamba utumiki wa nthawi zonse ali wachinyamata. M’funseni kuti, ‘Kodi n’chiyani chinakupangitsani kusankha kuchita zimenezi? Kodi mwapeza madalitso otani?’

Nyimbo Na. 72

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena