Ndandanda ya Mlungu wa March 16
MLUNGU WOYAMBIRA MARCH 16
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 16, ndime 1-11
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Genesis 43-46
Na. 1: Genesis 44: 1-17
Na. 2: Yesu Ali ndi Mphamvu Kuposa Ziwanda (lr-CN mutu 10)
Na. 3: Maulosi a Baibulo Atsimikizira Kukhala Odalirika Kotheratu (rs-CN tsamba 155, ndime 2-5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Yehova Amadziwika ndi Dzina Lake. Nkhani yokambidwa mwaumoyo yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, patsamba 274, ndime 2-5.
Mph. 10: “Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira.” Nkhani ndi kukambirana ndi omvera. Ngati nthawi ilipo, pemphani omvera kupereka ndemanga pa malemba omwe ali m’kalatayi.
Mph. 10: N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kusonkhana? Nkhani ndi kukambirana ndi omvera, yochokera mu Nsanja ya Olonda ya May 15, 2007, masamba 11-13. Pemphani omvera kuti afotokoze phindu limene apeza chifukwa chosonkhana komanso zimene amachita kuti azipezeka pamisonkhano mokhazikika ngakhale pali zolepheretsa zina.