Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 3/09 tsamba 2
  • Ndandanda ya Mlungu wa March 23

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa March 23
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2009
  • Timitu
  • Ndandanda ya Mlungu wa March 23
  • MLUNGU WOYAMBIRA MARCH 23
Utumiki Wathu wa Ufumu—2009
km 3/09 tsamba 2

Ndandanda ya Mlungu wa March 23

MLUNGU WOYAMBIRA MARCH 23

Nyimbo Na. 76

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

cl-CN mutu 16, ndime 12-22, ndi bokosi

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Genesis 47-50

Na. 1: Genesis 48:1-16

Na. 2: Kodi Mdyerekezi Tizimuopa?

Na. 3: Angelo a Mulungu Amatithandiza (lr-CN mutu 11)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 118

Mph. 5: Zilengezo.

Mph. 10: Konzekerani Kugawira Nsanja ya Olonda ya April 1 ndi Galamukani! ya April. Kukambirana ndi omvera. Pambuyo pofotokoza mwachidule zimene zili m’magaziniwo, pemphani omvera kuti atchule nkhani zimene akufuna kudzagwiritsira ntchito m’gawo lanu ndiponso chifukwa chake. Kodi angagwiritsire ntchito mafunso ndi malemba otani posonyeza nkhanizo? Chitani zitsanzo zosonyeza mmene tingagawirire magazini iliyonse. Mu chitsanzo chimodzi, musonyeze mmene tingayambitsire phunziro pa ulendo wobwereza.

Mph. 10: Zosowa za pampingo.

Mph. 10: Sonyezani Ulemu mwa Kumvetsera Mosamala ndi Kuganizira Malingaliro a Mwininyumba. Nkhani ndi kukambirana ndi omvera, yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, masamba 186-187. Chitani chitsanzo chosonyeza mmene tingagwiritsire ntchito malangizo amenewa. Kenako, pemphani omvera kuti afotokoze chifukwa chake akuganiza kuti zimene wofalitsa wachita m’chitsanzochi ndi zothandiza kwambiri.

Nyimbo Na. 89

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena