Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 1/14 tsamba 4
  • Ndandanda ya Mlungu wa February 3

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa February 3
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA FEBRUARY 3
Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
km 1/14 tsamba 4

Ndandanda ya Mlungu wa February 3

MLUNGU WOYAMBIRA FEBRUARY 3

Nyimbo Na. 76 ndi Pemphero

Phunziro la Baibulo la Mpingo:

jr mutu 7 ndime 1-6 (Mph. 30)

Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Genesis 21-24 (Mph. 10)

Na. 1: Genesis 23:1-20 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Chifukwa Chimene Yesu Ankavalira Matupi Anyama—rs tsa. 108 ndime 3–tsa. 109 ndime 2 (Mph. 5)

Na. 3: Khalani Ndi Chikhulupiriro Chimene Chimakondweretsa Mulungu—bh tsa. 176 ndime 5-7 (Mph. 5)

Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 81

Mph. 10: Zimene Munganene Pogawira Magazini a February. Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuchita chitsanzo cha mmene tingagawirire magaziniwo pogwiritsa ntchito zitsanzo za ulaliki zimene zili patsamba lino. Kenako werengani zitsanzo za ulalikizo. Muziwerenga chiganizo chimodzi kapena ziwiri n’kupempha omvera kuti afotokozepo. Chitani zimenezi mpaka mutamaliza kuwerenga mawu onse. Kumbutsani ofalitsa onse kuti azinena zimenezi m’mawu awoawo, akhoza kusintha chitsanzochi mwina ndi mwina kuti chigwirizane ndi mwininyumba kapenanso akhoza kukonza chitsanzo chawo. Pomaliza, limbikitsani ofalitsa onse kuti ayenera kuwerenga magaziniwo n’cholinga choti awadziwe bwino komanso alimbikitseni kuti adzagawire nawo magaziniwa.

Mph. 10: Zosowa za pampingo

Mph. 10: Mudzawazindikira Ndi Zipatso Zawo. (Mat. 7:16) Nkhani yokambirana yochokera mu Buku Lapachaka la 2013, tsamba 47 ndime 1-2 komanso tsamba 52 ndime 1-6. Pemphani omvera kuti anene zimene tikuphunzirapo.

Nyimbo Na. 25 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena