Zilengezo
◼ Mabuku ogawira mu January ndi February: Timabuku takuti, Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu, Mverani Mulungu, Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha, Mungathe Kukhala Bwenzi la Mulungu! ndi kakuti, Kodi Mulungu Amatisamaliradi? March ndi April: Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani!
◼ Tikukukumbutsani kuti mukamalemba malipoti a utumiki wakumunda, musamaphatikizepo chiwerengero cha timapepala toitanira anthu ku Chikumbutso, ku msonkhano wachigawo kapena timapepala tilitonse.