Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 6/13 tsamba 3
  • Ndandanda ya Mlungu wa July 1

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa July 1
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA JULY 1
Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
km 6/13 tsamba 3

Ndandanda ya Mlungu wa July 1

MLUNGU WOYAMBIRA JULY 1

Nyimbo Na. 83 ndi Pemphero

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

bt mutu 25 ndime 8-13 ndi bokosi patsamba 201 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Machitidwe 11–14 (Mph. 10)

Na. 1: Machitidwe 11:1-18 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Kodi Dipo Liyenera Kukhudza Bwanji Mmene Timachitira Zinthu pa Moyo Wathu?—rs tsamba 127 ndime 4 mpaka 6 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Mumakonda Kucheza Ndi Anthu Otani?—Sal. 119:63 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 120

Mph. 10: “Mvetserani ndi Kuphunzira.” Mafunso ndi Mayankho. Phatikizanipo zilengezo ziwiri za mu Utumiki wa Ufumu uno zokhudza msonkhano wachigawo.

Mph. 10: “Ntchito Imene Imathandiza Kwambiri.” Nkhani. Perekani kwa aliyense timapepala toitanira anthu kumsonkhano, ngati tilipo, ndipo kambiranani zomwe zili m’kapepalaka. Dziwitsani onse deti limene mpingo wanu udzayambe kugawa timapepalati ndipo fotokozani dongosolo limene lakonzedwa logawirira timapepalati m’gawo lanu. Chitani chitsanzo chachidule.

Mph. 10: “Khalidwe Lathu Labwino Limalemekeza Mulungu.” Mafunso ndi Mayankho. Kambirananinso mfundo zina pa mutu wakuti, “Zofunika Kukumbukira pa Msonkhano Wachigawo wa 2013.”

Nyimbo Na. 121 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena