Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 7/09 tsamba 3
  • Ndandanda ya Mlungu wa July 27

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa July 27
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2009
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA JULY 27
Utumiki Wathu wa Ufumu—2009
km 7/09 tsamba 3

Ndandanda ya Mlungu wa July 27

MLUNGU WOYAMBIRA JULY 27

Nyimbo Na. 77

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

cl-CN mutu 23 ndime 1-9

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Numeri 1-3

Na. 1: Numeri 3:1-20

Na. 2: Chifukwa Chake Kufatsa Kumafuna Kudziletsa

Na. 3: Kodi Mulungu Wanu Ndani? (lr-CN mutu 27)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 131

Mph.5: Zilengezo.

Mph.10: Gwiritsani Ntchito Mafunso Mwaluso. Kukambirana ndi omvera kuchokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, masamba 236 mpaka 237 ndime 2. Chitani chitsanzo mwachidule chosonyeza mmene tingagwiritsire ntchito mfundo imodzi kapena ziwiri za m’nkhaniyi.

Mph.10: Funsani makolo awiri kapena atatu a chitsanzo chabwino. Kodi amathana bwanji ndi mavuto amene amakumana nawo pochita utumiki monga banja? Kodi akuchita zotani pofuna kuthandiza ana awo kuti azikonda utumiki? Kodi akuchita zotani pa pulogalamu yawo ya Kulambira kwa Pabanja n’cholinga choti athandize ana awo kukonzekera utumiki?

Mph.10: “Lemekezani Yehova Tsiku Lililonse.” Kambiranani mwa mafunso ndi mayankho.

Nyimbo Na. 154

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena