Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 1997
Zosonyeza Deti la Kope Lopezekamo Nkhaniyo
ANACHITA CHIFUNIRO CHA YEHOVA
Amtama Yesu Kuti Ndiye Mesiya ndi Mfumu, 3/1
Chikhulupiriro cha Makolo Chifupidwa (makolo a Mose), 5/1
Chitsanzo cha Kudzimana ndi Kukhulupirika (Elisa), 11/1
Kupezera Isake Mkazi, 1/1
Mkazi Wanzeru Apeŵa Tsoka (Abigayeli), 7/1
Tate Yemwe Ali Wokonzeka Kukhululukira (fanizo la mwana woloŵerera), 9/1
BAIBULO
Baibulo la Makarios, 12/15
Buku Lapadera, 6/15
Kodi Mulungu Analiuzira Motani? 6/15
Mmene Baibulo Linadzafikira kwa Ife, 8/15, 9/15, 10/15
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
Chilango cha imfa, 6/15
Kodi mamvedwe atsopano a “mbadwo” (Mt 24:34) amakhudza 1914? 6/1
Kodi “mbadwo” (Mt 24:34) umapereka lingaliro lakuti mapeto ali kutali kwambiri? 5/1
Kodi Mboni lerolino zikuchitako ntchito yolekanitsa? 7/1
Kugwiritsira ntchito nsapo ndi ntchofu, 2/1
Malonda—nchifukwa ninji nkofunika kulemba pangano? 8/1
Otembenuka ‘pachisautso chachikulu’? 2/15
Pedophilia, 2/1
Tetragramatoni ya m’Mateyu wa Shem-Tob? 8/15
Upo wa ajuli, 4/1
MBONI ZA YEHOVA
‘Anagula Choonadi’! (Ghana), 12/15
Brosha Lakuti Mulungu Amafunanji, 1/15
Chilakiko ku Greece, 2/1
Chizunzo cha Anazi, 8/15
Khoti Yapamwamba ya ku Connecticut Ichirikiza Zoyenera za Odwala, 8/1
Kodi Nchifukwa Ninji Onse Ayenera Kutamanda Mulungu? (zokumana nazo), 1/1
Kuchezera Munda Wakwathu Waumishonale (C. Seymour), 6/15
Kukonda Osoŵa, 10/1
Kutsiriza Maphunziro a Gileadi, 6/1, 12/1
Kutsutsa Zinenezo ku France, 3/15
Kuwamasula Mwauzimu Andende (Mexico), 2/15
Misonkhano Yachigawo ya “Amithenga a Mtendere Waumulungu,” 1/15
Misonkhano ya Mitundu Yonse, 4/1
“Mmodzi mwa Anthu Ambiri Amene Munakhudza Mtima,” 3/1
Mwambo Wakuchiritsa ndi Opaleshoni Yopanda Mwazi, 2/15
Onga Nkhosa mu Dziko la Anavajo, 8/15
Uthenga Wabwino wa Paradaiso ku Tahiti, 10/15
Zopereka, 11/1
MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU
Chenjerani ndi “Aepikureya,” 11/1
Chenjerani ndi Kukayikira Zolinga za Ena, 5/15
Chikumbumtima, 8/1
Chiyembekezo Mutataya Mtima, 5/15
Kodi Kudandaula Konse Nkoipa? 12/1
Kodi Mukulakalaka Kuwonjezera Utumiki Wanu? 3/15
Kodi Mumadya Bwino Mwauzimu? 4/15
Kodi Mzimu wa Dziko Ukukuipitsani? 10/1
Kodi Ndinu Bwenzi la Mulungu?—Mapemphero Avumbula, 7/1
Kufooka kwa Anthu Kusonyeza Mphamvu ya Yehova, 6/1
Kukhulupirika, 5/1
Kulemekeza Makolo Okalamba, 9/1
Kuona Mtima—Mwamwaŵi Kapena Mosankha? 5/15
Kuopa Kukhulupirira Ena? 3/1
Kuzindikira Pulinsipulo, 10/15
“Lemekeza Yehova ndi Chuma Chako”—Motani? 11/1
Maukwati Olemekeza Yehova, 4/15
Nkuululiranji Choipa? 8/15
Phunziro la Banja, 8/1
Pulumutsani Moyo wa Mwana Wanu! 7/15
Sungani Chimwemwe mu Utumiki wa Nthaŵi Zonse, 9/15
Tidane Nacho Choipa, 1/1
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
Chidaliro Changa mwa Yehova Chinandichirikiza (A. Paixão), 2/1
Choonadi cha Baibulo Ndinachiphunzirira ku Romania (G. Romocean), 4/1
Kudikirabe Yehova Moleza Mtima Kuyambira Ubwana Wanga (R. Graichen), 8/1
Kulepa Zochuluka Chifukwa cha Kanthu Kena Kokulirapo (J. Owo Bello), 1/1
Mapindu a Utumiki Wopatulika (H. Bloor), 12/1
“M’Malo mwa Golidi, Ndinapeza Madiamondi” (M. Kaminaris), 3/1
Moyo Umene Sindinadandaulepo Nawo (P. Obrist), 7/1
Mtima Wanga Wadzaza Chiyamiko Chosaneneka (J. Wynn), 9/1
Mulungu Ndiye Pothaŵira Panga ndi Mphamvu Yanga (C. Müller), 5/1
Ndinaona “Wamng’ono” Akusanduka “Mtundu Wamphamvu” (W. Dingman), 11/1
Woyamikira Chifukwa Chotumikira Yehova Nthaŵi Yaitali (O. Mydland), 10/1
Yehova Amachita Mokhulupirika (P. Palliser), 6/1
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA
“Adalenga Iwo Mwamuna ndi Mkazi,” 6/15
Akristu ndi Dziko la Anthu, 11/1
“Amene Mungakhale Simunamuona Mumkonda,” 2/1
Amithenga a Mtendere Waumulungu Atchedwa Achimwemwe, 5/1
Chenjerani ndi Aphunzitsi Onama! 9/1
Chikhulupiriro Chimatipanga Kukhala Oleza Mtima ndi Olimbikira Kupemphera, 11/15
Chikhulupiriro Chimatisonkhezera Kuchitapo Kanthu! 11/15
Chikondi Chanu cha pa Abale Chikhalebe! 8/1
Chinsinsi Chimene Akristu Sayenera Kusunga! 6/1
“Choyenera Anthu Onse,” 2/15
Funafunani Mtendere Weniweni ndi Kuulondola! 4/15
Gwiritsitsani Chikhulupiriro Chanu Mosasamala Kanthu za Ziyeso! 11/15
Kodi Mudzakhulupirika Monga Eliya? 9/15
Kodi Mukulondola Khalidwe Labwino? 7/15
Kodi Mulungu Amafunanji kwa Ife? 1/15
Kodi Mwakonzekera Tsiku la Yehova? 3/1
Kodi Tikhalire Moyo Zalero Kapena Zamtsogolo Mosatha? 8/15
Kodi Ndani Adzapulumuka “Tsiku la Yehova”? 9/15
Kuchirikiza Mokhulupirika Mawu a Mulungu Ouziridwa, 10/1
Kudziŵa Mtundu Wabwino wa Mthenga, 5/1
Kukhala “Anzeru” Pamene Mapeto Ayandikira, 8/15
Kukhala m’Dziko Koma Osakhala Mbali Yake, 11/1
Kulanditsidwa ndi Kuloŵa m’Dziko Latsopano Lolungama, 4/1
Kumbukirani Tsiku la Yehova Nthaŵi Zonse, 9/1
Kupulumuka ‘Tsiku la Yehova,’ 12/15
Kusunga Khalidwe Labwino m’Dziko Lodzala ndi Makhalidwe Oipa, 7/15
Kuthandiza Ena Kuphunzira Zimene Mulungu Amafuna, 1/15
Kutumikira Limodzi ndi Gulu la Yehova Mokhulupirika, 8/1
Kutumikira Monga Amithenga a Mtendere Waumulungu, 1/15
Kuzindikira Kukuchinjirizeni, 3/15
Limbani Mtima Pamene Chilanditso Chikuyandikira, 4/1
Londolani Mtendere Waumulungu m’Moyo wa Banja, 6/15
Lozetsani Mtima Wanu ku Kuzindikira, 3/15
Madalitso a Utumiki Waupainiya, 10/15
Mawu a Mulungu Akhala Kosatha, 10/1
Moyo Wanu—Kodi Chifuno Chake Nchiyani? 2/15
Mtendere Weniweni—Kodi Udzachokera Kuti? 4/15
“Mulungu Anatikonda Ife Kotero,” 2/1
Odala Iwo Amene Adikira! 3/1
Onse Alemekeze Yehova! 1/1
Opatulidwa Kukhala Atamandi Achimwemwe pa Dziko Lonse, 7/1
Palibe Mtendere kwa Amithenga Onyenga! 5/1
Pamene Yesu Afika mu Ulemerero wa Ufumu, 5/15
Perekani Chilengezo Chapoyera cha Chipulumutso, 12/15
‘Pitirizani Kukhululukirana Eni Okha,’ 12/1
Tigwiritse Chikhulupiriro Chathu Chamtengo Wapatali! 9/1
Ulemerero Waukulu Kwambiri wa Nyumba ya Yehova, 1/1
Uyang’aniro Wateokrase m’Nthaŵi ya Akristu, 5/15
Yehova Amayamikira Utumiki Wanu wa Mtima Wonse, 10/15
Yehova, Mulungu “Wokhululukira,” 12/1
Yehova—Mulungu Wovumbula Zinsinsi, 6/1
“Yehova Sadzasiya Anthu Ake,” 7/1
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Achinyamata—Tsogolo Labwino? 12/1
Akatswiri Odumphadumpha m’Miyala ya m’Mapiri, 7/15
Aristarko, 9/15
Aumphaŵi Komabe Olemera, 9/15
Chimwemwe—Kodi Mfungulo Yake Nchiyani? 10/15
Chipulumutso, 8/15
Ehudi, 3/15
Enoke, 1/15
Epafra, 5/15
“Kachisi wa Mulungu” ndi Mafano m’Greece, 2/15
Kodi Chikhulupiriro Chimalira Chozizwitsa? 3/15
Kodi Chimwemwe Chingapezeke Kuti? 3/15
Kodi Madyerero a Kututa Amakondweretsa Mulungu? 9/15
Kodi Ozunzika Adzakhaladi ndi Mtendere? 4/15
Krisimasi, 12/15
Kubadwanso m’Moyo Wina, 5/15
Kuchiritsa, 7/1
Kufunitsitsa Dziko Lolungama? 11/15
Kukhalabe Namwali Muukwati? (Mariya), 10/15
Kukhulupirika m’Dziko Lopanda Ungwiro, 5/1
Kuumirira Mwambo, 3/1
“Kuweruza mwa Kufufuza”—Kodi Nchiphunzitso cha Baibulo? 7/15
Magulu Achinsinsi, 6/1
Malamulo Khumi, 12/1
“Malaya Opatulika a ku Trier,” 4/1
Malo a Nyimbo Pakulambira Kwamakono, 2/1
Masiku Otsiriza, 4/1
Mishnah, 11/15
Naḥmanides—Kodi Anatsutsa Chikristu? 4/15
Onesiforo, 11/15
Pamene Mavuto Sadzakhalakonso, 2/15
Sekemu—Mzinda wa m’Chigwa, 2/1
Sukulu Zaboding’i, 3/15
Sunemu—Wodziŵika ndi Chikondi ndi Chiwawa, 10/1
Tertio, 7/15
Uchimo, 7/15
Ufulu wa Chipembedzo, 2/1
Ukwati wa Zaka 403 Uli m’Vuto (Tchalitchi cha Sweden), 4/1
Umodzi wa Dziko Lonse, 11/1
Yerusalemu m’Nthaŵi za Baibulo, 6/15
Zozizwitsa Zokha Sizimabala Chikhulupiriro, 3/15
OLENGEZA UFUMU AKUSIMBA
2/1, 3/1, 4/1, 6/1, 7/1, 8/1, 9/1, 10/1, 12/1
YEHOVA
Amalamulira Mwachifundo, 12/15
“Mulungu wa Mtendere” Amawasamala Amene Akuzunzika, 4/15
Mulungu wa Umunthu Wake, 10/1
YESU KRISTU
Amtama Kuti Ndiye Mesiya ndi Mfumu, 3/1