Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w90 11/1 tsamba 32
  • Kodi Mungakonde Kuchezeredwa?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungakonde Kuchezeredwa?
  • Nsanja ya Olonda​—1990
Nsanja ya Olonda​—1990
w90 11/1 tsamba 32

Kodi Mungakonde Kuchezeredwa?

Mmodzi wa Mboni za Yehova angafune kukuchezerani ndi kukuthandizani kuwonjezera chidziŵitso chanu chonena za Mulungu, Ufumu wake, ndi zifuno zake, monga momwe zalembedwera m’Baibulo. Tiri achidaliro kuti chidziŵitso chimenechi chidzakuthandizani, popeza kuti chidzapereka mayankho odalirika amavuto amene tonsefe tikuyang’anizana nawo lerolino. Mboni za Yehova zimapereka chilangizo cha m’Baibulo kwa aliyense payekha ndi kugulu popanda malipiro.

Chotero ngati mungafune kuchezeredwa ndi munthu woyeneretsedwa panyumba panu, kapena pamalo ena oyenerera, tidzakhala osangalala kukupangirani makonzedwe. Mudzathandizidwa kupeza osati kokha mayankho a mafunso anu a Baibulo komanso mayankho a mavuto alerolino amene angathetsedwe mwakugwiritsira ntchito malamulo amakhalidwe abwino a Baibulo. Kuti mupindule inu eni ndi utumiki umenewu, tangolembani mawu ofunidwa pansipa ndi kutumiza ku keyala iri pakapepalaka.

Ndingakonde kudziŵa zowonjezereka ponena za Baibulo. Chonde linganizani kuti wina adzandichezere.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena