Tsamba 2
Kodi Mungadalire Yani? 3-10
Anthu owonjezereka amaona kudalira ena kukhala kovuta. Chifukwa ninji? Kodi tingapeŵe motani kuika chidaliro chathu pamalo olakwika?
Thambo Lodabwitsa 19-30
Kodi nchifukwa ninji tili pano? Kodi tikumka kuti? Kodi chifuno chake nchiyani? Kodi chiphunzitso cha big bang chimafotokoza mmene chilengedwe chinakhalirako?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Mwachilolezo cha ROE/Anglo-Australian Observatory, chojambulidwa ndi David Malin