Tsamba 2
Pamene Sikudzakhalanso Matenda 3-14
Anthu kulikonse amasamala za thanzi lawo. Ŵerengani za nthaŵi imene ikudza posachedwapa pamene banja laumunthu lidzakhala ndi thanzi labwino.
Kuzengereza—Mbala ya Nthaŵi 18
Kodi mungathetse motani chizoloŵezi cha kuzengereza zinthu zimene ziyenera kuchitidwa mwamsanga?