Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 7/15 tsamba 8
  • Ndandanda ya Mlungu wa August 3

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa August 3
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA AUGUST 3
Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
km 7/15 tsamba 8

Ndandanda ya Mlungu wa August 3

MLUNGU WOYAMBIRA AUGUST 3

Nyimbo Na. 48 ndi Pemphero

Phunziro la Baibulo la Mpingo:

cl mutu 16 ndime 18-22 ndi bokosi patsamba 167 (30 min.)

Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: 1 Mafumu 18-20 (8 min.)

Na. 1: 1 Mafumu 18:30-40 (Osapitirira 3 min.)

Na. 2: Akazi Okhulupirira Amatamanda Yehova—bt bokosi tsa. 132 (5 min.)

Na. 3: Kodi Baibulo Lingathandize Bwanji Ana?—igw tsa. 27 ndime 1-2 (5 min.)

Msonkhano wa Utumiki:

Mutu wa Mwezi Uno: ‘Pitani mukaphunzitse anthu kuti akhale ophunzira anga.’—Mat. 28:19, 20.

Nyimbo Na. 130

10 min: Zimene Munganene Pogawira Magazini a August. Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuchita zitsanzo zosonyeza zimene tinganene pogawira magaziniwa, pogwiritsa ntchito zitsanzo zaulaliki zomwe zili patsamba lino. Kenako kambiranani chitsanzo cha ulaliki chilichonse kuyambira poyambirira mpaka pamapeto.

10 min: Muzigwiritsa Ntchito Kabuku Kakuti, Kuphunzira Malemba Tsiku ndi Tsiku. Nkhani yokambirana. Yambani ndi kukamba nkhani ya 5 minitsi yochokera pa lemba la chaka cha 2015. Kenako pemphani omvera kuti anene nthawi imene amapanga lemba la tsiku. Pomaliza limbikitsani onse kuti tsiku lililonse azichita lemba la tsiku pogwiritsa ntchito kabukuka.

10 min: Zofunika pampingo.

Nyimbo Na. 26 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena