Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 5/15 tsamba 1
  • Ndandanda ya Mlungu wa May 11

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa May 11
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA MAY 11
Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
km 5/15 tsamba 1

Ndandanda ya Mlungu wa May 11

MLUNGU WOYAMBIRA MAY 11

Nyimbo Na. 133 ndi Pemphero

Phunziro la Baibulo la Mpingo:

cl mutu 12 ndime 16-21 ndi bokosi patsamba 127 (30 min.)

Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: 2 Samueli 4-8 (8 min.)

Na. 1: 2 Samueli 6:14-23 (Osapitirira 3 min.)

Na. 2: Kodi Chimachitika N’chiyani Munthu Akamwalira?—igw tsa. 18 ndime 1-3 (5 min.)

Na. 3: Khalani Odzichepetsa Kuti Musakumane ndi Tsoka Ngati Belisazara—dp tsa. 110 ndime 23-24 (5 min.)

Msonkhano wa Utumiki:

Mutu wa Mwezi Uno: Muzithandiza anthu onse kudziwa choonadi molondola.—1 Tim. 2:3, 4.

Nyimbo Na. 92

10 min: Muzithandiza Anthu Onse Kudziwa Choonadi Molondola. Nkhani yochokera pa mutu wa mwezi uno. (Onani Nsanja ya Olonda ya November 15, 2013, tsa. 11-12 ndime 8.) Werengani ndi kukambirana lemba la 1 Timoteyo 2:3, 4 komanso 1 Akorinto 9:19-23. Tchulani nkhani zomwe tiphunzire mu Msonkhano wa Utumiki mwezi uno ndipo fotokozani kugwirizana kwa nkhanizo ndi mutu wa mwezi uno.

20 min: “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Muzilalikira Anthu Oyankhula Chinenero China.” Nkhani yokambirana. Chitani chitsanzo chachidule chosonyeza wofalitsa akugwiritsa ntchito kabuku ka Uthenga Wabwino wa Anthu a Mitundu Yonse polalikira munthu wachinenero china yemwe wakumana naye pamene amalalikira kunyumba ndi nyumba.

Nyimbo Na. 105 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena