Ndandanda ya Mlungu wa January 5
MLUNGU WOYAMBIRA JANUARY 5, 2015
Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero
Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 6 ndime 16-21 ndi bokosi patsamba 65 (Mph. 30)
Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yoswa 16-20 (Mph. 8)
Na. 1: Yoswa 17:11-18 (Osapitirira mph. 3)
Na. 2: Kodi Mulungu Ndi Ndani?—igw tsa. 2 ndime 1-3 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Tiyenera Kupewa Chiyani Ngati Zikutiyendera Bwino mu Utumiki?—bt tsa. 29-31 ndime 5-8 (Mph. 5)
Msonkhano wa Utumiki:
Mutu wa Mwezi Uno: Tizipereka zinthu “zabwino” zochokera m’chuma chomwe tinapatsidwa.—Mat. 12:35a.
Mph. 30: “Nyimbo Zatsopano.” Onani tsamba 7. Nkhani yokambirana. Mukamakambirana ndime 6, ikani nyimbo yatsopano ya mutu wakuti, “Ufumu Umene Ukulamulira Kumwamba Ubwere.” Pemphani omvera kuti aimirire ndi kuimba nyimboyi. Mungaimbe nyimboyi kawiri kuti anthu aizolowere. Ngati simungathe kupita pa webusaiti ya jw.org kuti muchite dawunilodi nyimboyi, muimbe nyimbo nambala 108 yakuti, “Tamandani Yehova Chifukwa cha Ufumu Wake.”
Nyimbo yatsopano ya mutu wakuti, “Ufumu Umene Ukulamulira Kumwamba Ubwere” ndi Pemphero