Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 11/14 tsamba 4
  • Ndandanda ya Mlungu wa December 1

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa December 1
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA DECEMBER 1
Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
km 11/14 tsamba 4

Ndandanda ya Mlungu wa December 1

MLUNGU WOYAMBIRA DECEMBER 1

Nyimbo Na. 105 ndi Pemphero

Phunziro la Baibulo la Mpingo:

cl mutu 5 ndime 1-8 (Mph. 30)

Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Deuteronomo 32-34 (Mph. 10)

Na. 1: Deuteronomo 32:22-35 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Munthu Akafa, Mzimu Wake Kapena Kuti Moyo Wake Supitirizanso Kukhala Ndi Moyo—rs tsa. 297 ndime 1–tsa. 299 ndime 3 (Mph. 5)

Na. 3: Kuchita Chigololo Ndi Kuchimwira Mulungu—lv tsa. 128-129 ndime 16-19 (Mph. 5)

Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 128

Mph. 10: Zimene Munganene Pogawira Magazini a December. Nkhani yokambirana. Chitani zitsanzo zitatu zomwe zili patsamba lino. Mukamaliza kuchita chitsanzo chilichonse, pemphani omvera kuti afotokoze chifukwa chake anthu ambiri a m’gawo lanu angakhale ndi chidwi ndi nkhanizi.

Mph. 10: Zofunika pampingo.

Mph. 10: Kodi Tinachita Zotani? Nkhani yokambirana. Pemphani omvera kuti afotokoze phindu lomwe apeza pogwiritsa ntchito malangizo a m’nkhani yakuti, “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Muzisonyeza Chidwi Munthu Amene Mukumulalikira.” Apempheninso kuti afotokoze zinthu zosangalatsa zomwe zinachitika pomwe ankagwiritsa ntchito mfundo za m’nkhaniyi.

Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena