Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 10/14 tsamba 1
  • Ndandanda ya Mlungu wa October 13

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa October 13
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA OCTOBER 13
Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
km 10/14 tsamba 1

Ndandanda ya Mlungu wa October 13

MLUNGU WOYAMBIRA OCTOBER 13

Nyimbo Na. 57 ndi Pemphero

Phunziro la Baibulo la Mpingo:

cl mutu 2 ndime 21-24 ndi bokosi patsamba 24 (Mph. 30)

Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Deuteronomo 4-6 (Mph. 10)

Na. 1: Deuteronomo 4:29-43 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Zimene Anthu Ayenera Kusintha Kuti Asangalatse Mulungu—rs tsa. 181 ndime 3–tsa. 182 ndime 1 (Mph. 5)

Na. 3: Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani Yogonana Amuna Kapena Akazi Okhaokha—rs tsa. 180 ndime 5–tsa. 181 ndime 2 (Mph. 5)

Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 92

Mph. 5: Kulalikira Modzipereka. Nkhani yolimbikitsa yochokera pa 2 Timoteyo 4:2. Gwiritsani ntchito mfundo zomwe zili mu Nsanja ya Olonda ya March 15, 2012, patsamba 16 ndi 17, ndime 7 mpaka 9.

Mph. 10: N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kulalikira Modzipereka? Nkhani yokambidwa ndi mkulu yochokera mu Nsanja ya Olonda ya March 15, 2012, tsamba 15 ndi 16, ndime 3 mpaka 6 komanso tsamba 18 ndime 14 mpaka 18. Tchulani mmene mfundo zochokera mu nkhani za mu Utumiki wa Ufumu za mutu wakuti, “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki” zingatithandizire kuti tizilalikira modzipereka.

Mph. 15: “Muzigwiritsa Ntchito Mpata Uliwonse Kulalikira Uthenga wa Ufumu.” Mafunso ndi mayankho. Mukamakambirana ndime 3, pemphani omvera kuti afotokoze zinthu zosangalatsa zomwe zinachitika pamene ankalalikira mwamwayi. Pomaliza, tchulani mmene mfundo za m’nkhaniyi zikugwirizanirana ndi mutu wa mwezi uno, ndipo limbikitsani omvera kuti akawerenge nkhani ziwiri za mutu wakuti, “Kucheza Ndi Munthu Wina” zimene tidzakambirane pa Msonkhano wa Utumiki wa mlungu wotsatira.

Nyimbo Na. 97 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena