Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 4/14 tsamba 1
  • Ndandanda ya Mlungu wa April 14

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa April 14
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA APRIL 14
Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
km 4/14 tsamba 1

Ndandanda ya Mlungu wa April 14

MLUNGU WOYAMBIRA APRIL 14

Nyimbo Na. 68 ndi Pemphero

Phunziro la Baibulo la Mpingo:

jr mutu 10 ndime 8-13 (Mph. 30)

Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Ekisodo 11-14 (Mph. 10)

Na. 1: Ekisodo 12:37-51 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Zinthu Zina Zimene Zimasonyeza Kukhalapo kwa Khristu—rs tsa. 165 ndime 1-5 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Satana Amafalitsa Mabodza Ati Okhudza Machimo Akuluakulu?—lv tsa. 164 ndime 1-4 (Mph. 5)

Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 100

Mph. 15: Werengani Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2014. Nkhani yokambirana. Kambiranani “Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira.” Muuziretu ofalitsa ena kuti adzafotokoze zochitika zochititsa chidwi za mu Buku Lapachaka limeneli, zomwe n’zolimbikitsa kwambiri. Pemphani omvera kuti afotokoze ziwerengero zochititsa chidwi zomwe zikupezeka m’lipoti lapadziko lonse la Mboni za Yehova. Pomaliza, limbikitsani anthu onse kuti awerenge Buku Lapachaka limeneli.

Mph. 15: “Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Muzithandiza Mnzanu Amene Mwayenda Naye.” Nkhani yokambirana. Chitani zitsanzo ziwiri zachidule zosonyeza munthu amene wayenda ndi mnzake mu utumiki koma sakumuthandiza. Pamapeto pa chitsanzo chilichonse, pemphani omvera kuti afotokoze zimene munthuyo anayenera kuchita.

Nyimbo Na. 45 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena