Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 1/14 tsamba 2
  • Ndandanda ya Mlungu wa January 20

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa January 20
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA JANUARY 20
Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
km 1/14 tsamba 2

Ndandanda ya Mlungu wa January 20

MLUNGU WOYAMBIRA JANUARY 20

Nyimbo Na. 68 ndi Pemphero

Phunziro la Baibulo la Mpingo:

jr mutu 6 ndime 13-18 ndi bokosi patsamba 74 (Mph. 30)

Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Genesis 11-16 (Mph. 10)

Na. 1: Genesis 14:17-24-15:1-11 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Mmene Mungayankhire Ngati Wina Wanena Kuti, ‘N’chiyani Chimene Chimakuchititsani Kuganiza Kuti Pali Chipembedzo Chimodzi Chokha Choona?’—rs tsa. 93 ndime 3 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Abadoni, Amene Ndi Mngelo wa Phompho Ndi Ndani?—re tsa. 148 ndime 20 (Mph. 5)

Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 123

Mph. 10: Kodi Tikuphunzirapo Chiyani? Nkhani. Werengani Mateyu 7:6-11 ndipo kambiranani mmene mavesi amenewa angatithandizire mu utumiki. Kambirananinso nkhani yakuti, “Zochitika mu Utumiki Wakumunda” patsamba 4.

Mph. 10: Muzilemekeza Anthu Amene Akugwira Ntchito Mwakhama Pakati Panu. (1 Ates. 5:12, 13) Nkhani yokambirana pogwiritsa ntchito mafunso otsatirawa: (1) Kodi akulu amagwira ntchito mwakhama mu mpingo m’njira ziti? (2) Kodi tingasonyeze bwanji kuti timalemekeza kwambiri akulu? (3) N’chifukwa chiyani anthu amene amatsogolera amafunikanso kuwalimbikitsa? (4) Kodi tingalimbikitse bwanji akulu komanso anthu a m’banja lawo? (5) Kodi kumvera amene akutitsogolera kumapindulitsa bwanji mpingo komanso akulu?

Mph. 10: “Muzilimbikitsa Mnzanu Amene Mwalowa Naye mu Utumiki.” Mafunso ndi mayankho. Pemphani omvera kuti afotokoze zinthu zothandiza zimene anaphunzira atayenda ndi munthu wina mu utumiki.

Nyimbo Na. 93 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena