Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 12/13 tsamba 2
  • Ndandanda ya Mlungu wa December 16

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa December 16
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA DECEMBER 16
Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
km 12/13 tsamba 2

Ndandanda ya Mlungu wa December 16

MLUNGU WOYAMBIRA DECEMBER 16

Nyimbo Na. 70 ndi Pemphero

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

jr mutu 5 ndime1-6 ndi bokosi patsamba 55 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Chivumbulutso 1-6 (Mph. 10)

Na. 1: Chivumbulutso 3:14–22 ndi 4:1-8 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Chipembedzo Choona Sichichita Zinthu Mwamwambo—rs tsa. 90 ndime 1 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Yesu Anapatsa Bwanji “Chitsanzo” Ophunzira Ake?—Yoh. 13:15 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 44

Mph. 10: Kodi Tinachita Zotani? Nkhani yokambirana yokambidwa ndi woyang’anira utumiki. Fotokozani mmene ntchito yogawira Uthenga wa Ufumu Na. 38 inayendera. Pemphani omvera kuti afotokoze mmene anapindulira pogwira nawo ntchito yogawira timapepalati ndiponso zinthu zosangalatsa zimene anakumana nazo.

Mph. 10: Achinyamata, Tamandani Yehova (Sal. 148:12, 13) Funsani achinyamata awiri kapena atatu achitsanzo chabwino. Kodi amakumana ndi mavuto otani kusukulu oyesa chikhulupiriro chawo? Kodi makolo awo komanso anthu ena awathandiza bwanji kuthana ndi mavuto amenewa? Nanga n’chiyani chimawathandiza kuti azilimba mtima kuuza ena zimene amakhulupirira? Apempheni kuti afotokoze zimene anakumana nazo.

Mph. 10: Bokosi la Mafunso. Nkhani yokambirana.

Nyimbo Na. 75 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena