Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 7/13 tsamba 1
  • Ndandanda ya Mlungu wa July 8

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa July 8
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA JULY 8
Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
km 7/13 tsamba 1

Ndandanda ya Mlungu wa July 8

MLUNGU WOYAMBIRA JULY 8

Nyimbo Na. 100 ndi Pemphero

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

bt mutu 25 ndime 14-21 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Machitidwe 15–17 (Mph. 10)

Na. 1: Machitidwe 16:16-34 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: N’chifukwa Chiyani Mkhristu Ayenera Kusangalala Akamazunzidwa?—Mat. 5:11,12 (Mph. 5)

Na. 3: Pomwe Mtumwi Paulo Ananena Kuti Akhristu ‘Adzatengedwa’ Kukakhala ndi Ambuye, Kodi Ankafotokoza Nkhani Yanji?—rs tsa. 213 ndime 1-2 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 75

Mph. 10: Njira Zolalikirira Uthenga Wabwino—Kutsogolera Anthu Achidwi ku Gulu la Yehova. Nkhani yochokera m’buku la Gulu, tsamba 99, ndime 2 mpaka tsamba 100, ndime 1. Pemphani omvera kuti afotokoze mmene agwiritsira ntchito kabuku kakuti Kodi Ndani Akuchita Chifuniro cha Yehova? kuthandiza ophunzira awo kudziwa gulu la Yehova.

Mph. 10: Muyeseni Yehova, Ndipo Mudzalandira Madalitso Oti Mudzasowa Powalandirira (Mal. 3:10) Funsani apainiya okhazikika awiri kapena atatu. N’chiyani chimawasangalatsa kwambiri pa utumiki waupainiya? Nanga utumikiwu wawathandiza bwanji mwauzimu? Apempheni kuti afotokoze zinthu zosangalatsa zimene akumana nazo pochita utumikiwu. Pomaliza limbikitsani ofalitsa kuganizira ngati angathe kuyamba upainiya wokhazikika mu September.

Mph. 10: “Tengerani Chitsanzo kwa Aneneri—Yoweli.” Mafunso ndi Mayankho.

Nyimbo Na. 54 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena