Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 6/13 tsamba 2
  • Ndandanda ya Mlungu wa June 17

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa June 17
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA JUNE 17
Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
km 6/13 tsamba 2

Ndandanda ya Mlungu wa June 17

MLUNGU WOYAMBIRA JUNE 17

Nyimbo Na. 60 ndi Pemphero

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

bt mutu 24 ndime 16-21 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Machitidwe 5–7 (Mph. 10)

Na. 1: Machitidwe 5:17-32 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Kodi Munthu Angatani Kuti Azidziwidwa Ndi Yehova?—2 Tim. 2:19 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Tiyenera Kuchita chiyani Kuti Tipindule Kosatha Ndi Nsembe ya Yesu?​—rs tsa. 126 ndime 5 mpaka tsa. 127 ndime 1 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 61

Mph. 10: Kodi Tingasonyeze Bwanji Ulemu Tikakhala mu Utumiki? Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 190 ndime 1, mpaka tsamba 192 ndime 1. Chitani chitsanzo chachidule cha wofalitsa akulalikira mopanda ulemu kwa mwininyumba. Ndiyeno abwerezenso chitsanzocho koma pa nthawiyi asonyeze kuti akulemekeza mwininyumbayo.

Mph 10: Thandizani Omwe Mumaphunzira Nawo Kuti Akhale Ofalitsa. NKhani yochokera m’buku la Gulu tsamba 78 ndime 3, mpaka pakadontho komaliza patsamba 80.

Mph. 10: “Mwayi Winanso Wotamanda Yehova.” Mafunso ndi mayankho. Mwachidule funsani wofalitsa mmodzi kapena awiri omwe anachita upainiya wothandiza pa nthawi imene woyang’anira dera ankachezera mpingo wanu.

Nyimbo Na. 9 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena