Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 11/10 tsamba 8
  • Ndandanda ya Mlungu wa December 6

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa December 6
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2010
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA DECEMBER 6
Utumiki Wathu wa Ufumu—2010
km 11/10 tsamba 8

Ndandanda ya Mlungu wa December 6

MLUNGU WOYAMBIRA DECEMBER 6

Nyimbo Na. 21

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

lv mutu 16 ndime 1-9

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: 2 Mbiri 10-14

Na. 1: 2 Mbiri 13:1-12

Na. 2: Kodi Yehova Amateteza Motani Atumiki Ake Okondedwa Kapena Kuti Okhulupirika? (Sal. 37:28)

Na. 3: **Ngati Wina Anena Kuti: “N’chifukwa Chiyani Simuchita Nawo Zinthu Zothandiza Kuti Dzikoli Likhale Labwino Kwambiri?” (rs tsa. 278 ndime 4–tsa. 279 ndime 3)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 28

Mph. 10: Zilengezo. Pemphani omvera kuti afotokoze zokumana nazo pogawira kapena kuyambitsa maphunziro a Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?

Mph. 10: Zosowa za pampingo.

Mph. 15: Mmene Mungalemekezere Ena mu Utumiki. Nkhani yokambirana ndi omvera yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 190 mpaka 192, ndime 2.

Nyimbo Na. 32

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena