Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 10/10 tsamba 2
  • Ndandanda ya Mlungu wa October 18

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa October 18
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2010
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA OCTOBER 18
Utumiki Wathu wa Ufumu—2010
km 10/10 tsamba 2

Ndandanda ya Mlungu wa October 18

MLUNGU WOYAMBIRA OCTOBER 18

Nyimbo Na. 45

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

lv mutu 13 ndime 15-25 ndi bokosi patsamba 156a

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: 1 Mbiri 8-11

Na. 1: 1 Mbiri 11:1-14

Na. 2: Kodi Mzimu ndi Mkwatibwi Amanena Kuti, “Bwera,” M’njira Ziti? (Chiv. 22:17)

Na. 3: Kodi Mboni za Yehova Zimakhulupirira Kuti Chipembedzo Chawo Ndicho Chokha Cholondola? (rs tsa. 275 ndime 1 ndi 2)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 32

Mph. 5: Zilengezo.

Mph. 10: Chifukwa Chake Kuyang’ana Omvera mu Utumiki N’kofunika. Nkhani yokambirana ndi omvera yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 124, ndime 1, mpaka tsamba 125, ndime 4.

Mph. 20: “Kabuku Katsopano Kamene Tidzagawira.” Nkhani ya mafunso ndi mayankho. Pokambirana ndime 1, fotokozani mwachidule zimene zili m’kabukuka. Mukamaliza kukambirana ndime 2 ndi 3, chitani chitsanzo chosonyeza njira zolalikirira zomwe zatchulidwa mu ndimezo. Pambuyo pokambirana ndime 4, chitani chitsanzo chosonyeza mmene tingayambitsire phunziro la Baibulo la panyumba pa ulendo wobwereza.

Nyimbo Na. 37

[Mawu a M’munsi]

a Mungasankhe kukambirana bokosi kapena ayi.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena