Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 10/10 tsamba 1
  • Ndandanda ya Mlungu wa October 11

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa October 11
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2010
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA OCTOBER 11
Utumiki Wathu wa Ufumu—2010
km 10/10 tsamba 1

Ndandanda ya Mlungu wa October 11

MLUNGU WOYAMBIRA OCTOBER 11

Nyimbo Na. 50

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

lv mutu 13 ndime 5-14, ndi bokosi patsamba 150a

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: 1 Mbiri 5-7

Na. 1: 1 Mbiri 6:31-47

Na. 2: Kodi Mboni za Yehova Ndi Kagulu Kampatuko, Nanga Chipembedzo Chawo Chakhalapo kwa Utali Wotani? (rs tsa. 273 ndime 4–tsa. 274 ndime 4)

Na. 3: Kodi Zingatheke Bwanji Kuti Anthu Opanda Ungwiro Akhale Oyera? (1 Pet. 1:16)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 54

Mph. 5: Zilengezo.

Mph. 10: Kodi Muyenera Kuyankha Bwanji? Nkhani yokambirana ndi omvera yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 69, ndime 1-5. Khalani ndi chitsanzo chosonyeza mpainiya akuyankha munthu amene amaphunzira naye Baibulo yemwe akufunika kupanga chosankha. Wophunzirayo akufunsa kuti: “Kodi mukanakhala inuyo mukanatani pamenepa?”

Mph. 10: Kukhala Waukhondo Kumalemekeza Mulungu. Nkhani yochokera m’buku la Gulu, tsamba 137, ndime 1, mpaka tsamba 138, ndime 2. Pemphani omvera kuti afotokoze mmene ukhondo ndiponso kuoneka bwino kwa Mboni za Yehova kunawathandizira kuphunzira choonadi.

Mph. 10: “Musachite Mantha.” Nkhani ya mafunso ndi mayankho.

Nyimbo Na. 51

[Mawu a M’munsi]

a Mungasankhe kukambirana bokosi kapena ayi.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena