Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 12/09 tsamba 4
  • Ndandanda ya Mlungu wa January 4

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa January 4
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2009
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA JANUARY 4
Utumiki Wathu wa Ufumu—2009
km 12/09 tsamba 4

Ndandanda ya Mlungu wa January 4

MLUNGU WOYAMBIRA JANUARY 4

Nyimbo Na. 1

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

lv-CN mutu 1 ndime 1-9 ndiponso mawu oyamba

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Yoswa 16–20

Na. 1: Yoswa 17:1-10

Na. 2: Kodi Anthu Opita Kumwamba Akachitako Chiyani? (rs-CN tsa. 210 ndime 1 mpaka 5)

Na. 3: Kodi N’chifukwa Chiyani Munthu ‘Wokaikakaika’ Sasangalatsa Mulungu? (1 Maf. 18:21)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 45

Mph. 5: Zilengezo.

Mph. 10: Muzigwiritsa Ntchito Mafunso Kuti Muziphunzitsa Mogwira Mtima. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 239.

Mph. 10: Zosowa za pampingo.

Mph. 10: Muzigwiritsa Ntchito Mabuku Ofotokoza za M’Baibulo mu Utumiki Wanu. Kambiranani ndi omvera ndime zitatu za pamutu wakuti “Kugwiritsa Ntchito Mabuku Ofotokoza za M’Baibulo,” tsamba 100 ndi 101 m’buku la Gulu. Pemphani woyang’anira utumiki kapena mkulu wina kuti afotokoze mmene tingamagwiritsire ntchito mosamala mabuku athu.

Nyimbo Na. 47

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena