Ndandanda ya Mlungu wa June 8
MLUNGU WOYAMBIRA JUNE 8
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 20 ndime 13-21 ndi bokosi la patsamba 207
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Levitiko 1-5
Na. 1: Levitiko 4:1-15
Na. 2: Kodi Tiyenera Kudzitama Tikachita Zabwino? (lr-CN mutu 21)
Na. 3: Kodi Akhristu Ayenera Kugwiritsa Ntchito Bwanji Ulamuliro?
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph.5: Zilengezo.
Mph.10: Mbali ya Yesu Yofunika Kwambiri pa Chifuniro cha Mulungu. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, pamutu waung’ono patsamba 276.
Mph.10: Buku Logawira mu June. Chitani chitsanzo chimene chakhala chogwira mtima polalikira anthu a m’gawo lanu. Komanso sonyezani mmene mungagwiritsire ntchito bukulo poyambitsa phunziro la Baibulo.
Mph.10: “Timasonyeza Kuti Timakonda Mulungu mwa Utumiki Wathu.” Kambiranani mwa mafunso ndi mayankho.