Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 4/09 tsamba 1
  • Ndandanda ya Mlungu wa April 13

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa April 13
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2009
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA APRIL 13
Utumiki Wathu wa Ufumu—2009
km 4/09 tsamba 1

Ndandanda ya Mlungu wa April 13

MLUNGU WOYAMBIRA APRIL 13

Nyimbo Na. 38

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

cl-CN mutu 17, ndime 15-23 ndi bokosi

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Eksodo 11-14

Na. 1: Eksodo 12:21-36

Na. 2: Chifukwa Chake Tiyenera Kukhululukira Ena (lr-CN mutu 14)

Na. 3: Kodi Kuchiritsa Kumene Kumachitika Masiku Ano N’kosiyana Bwanji ndi Kuchiritsa kwa Yesu ndi Ophunzira Ake? (rs-CN tsa. 167 ndime 1–4)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 125

Mph.5: Zilengezo.

Mph.10: Fotokozani mmene zinthu zayendera patsiku lapadera loyambitsa maphunziro a Baibulo. Nenani chinthu chimodzi kapena ziwiri zimene zinachitika pogwira ntchitoyi m’gawo lanu.

Mph.10: Khalani Wosamala Polalikira. Kukambirana ndi omvera pogwiritsa ntchito mfundo za pakamutu ka patsamba 197 m’buku la Sukulu ya Utumiki. Chitani chitsanzo chosonyeza mmene wofalitsa angayankhire ngati mwininyumba wanena mfundo inayake imene anthu ambiri amanena pofuna kutitsutsa.

Mph.10: “Kulalikira Kumatilimbitsa Mwauzimu.” Nkhani ya mafunso ndi mayankho.

Nyimbo Na. 5

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena