Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 1/09 tsamba 1
  • Ndandanda ya Mlungu wa January 12

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa January 12
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2009
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA JANUARY 12
Utumiki Wathu wa Ufumu—2009
km 1/09 tsamba 1

Ndandanda ya Mlungu wa January 12

MLUNGU WOYAMBIRA JANUARY 12

Nyimbo Na. 162

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

cl-CN mutu 12, ndime 12-21 ndi bokosi

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Genesis 6-10

Na. 1: Genesis 9:1-17

Na. 2: Kuyankha Anthu Amene Amanena Kuti Sakhulupirira Mulungu (rs-CN tsa. 311 ndime 4 mpaka tsa. 312 ndime 2)

Na. 3: Kalata Yochokera kwa Mulungu Amene Amatikonda (lr-CN mutu 2)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 16

Mph. 5: Zilengezo za pampingo.

Mph. 10: Phindu Lokhala ndi Maganizo Abwino Muutumiki. Kukambirana ndi omvera. Yesu ankaona kuti anthu amene ankawalalikira anali ngati nkhosa zofunika kuthandizidwa ndipo chimenechi ndi chitsanzo chabwino kwa ife. (Mat. 9:36-38) Hananiya atauzidwa kuti akakumane ndi Saulo, anakayikira koma kenako anasintha. Kodi n’chiyani chinamuthandiza kusintha maganizo? (Mac. 9:13-15) Kodi zimene ananena atafika kwa Saulo zikusonyeza bwanji kuti Hananiya anali ndi maganizo abwino? (Mac. 9:17) Kodi n’chifukwa chiyani tiyenera kukhala ndi maganizo abwino tikamakambirana ndi anthu a m’gawo lathu? Kodi kukhala ndi maganizo abwino kungathandize bwanji kuti utumiki wathu ukhale wobala zipatso? Funsani wofalitsa mmodzi kapena awiri kuti afotokoze mwachidule mmene kukhala ndi maganizo abwino kunathandizira kuti utumiki wawo ukhale ndi zotsatira zabwino.

Mph. 10: Kodi Buku la Kukambitsirana za m’Malemba Tingaligwiritse Ntchito Bwanji? Nkhani yokambidwa ndi woyang’anira utumiki kapena mkulu wina aliyense, yochokera m’buku la Kukambitsirana, tsamba 7 ndi 8.

Mph. 10: “Adzamva Bwanji?”a

Nyimbo Na. 38

[Mawu a M’munsi]

a Mawu anu oyamba asafike mphindi imodzi, ndiyeno kambiranani mwa mafunso ndi mayankho.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena