Zamkatimu
October 15, 2009
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
November 30, 2009–December 6, 2009
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 191, 177
December 7-13, 2009
‘Khalani Mwamtendere ndi Anthu Onse’
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 159, 206
December 14-20, 2009
TSAMBA 13
NYIMBO ZOIMBA: 224, 217
December 21-27, 2009
Mungathe Kukhalabe ndi Mabwenzi M’dziko Lopanda Chikondi Lino
TSAMBA 17
NYIMBO ZOIMBA: 173, 155
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 3-11
Nkhani zimenezi zikufotokoza mavesi onse a Aroma chaputala 12, malinga ndi mfundo za m’mavesiwo. Tikambirana zimene mawu akuti “yakani ndi mzimu” amatanthauza ndiponso mmene tingaperekere matupi athu nsembe yamoyo kwa Mulungu. Tiphunziranso mmene tingalimbikitsire mtendere panyumba ndi mumpingo, ndiponso mmene tingagonjetsere choipa mwa kuchita chabwino.
Nkhani Zophunzira 3, 4 MASAMBA 13-21
Kodi kukhala bwenzi labwino kumatanthauza chiyani? Nkhani zimenezi zitithandiza kuona chitsanzo chabwino chimene Yesu anapereka pa nkhani imeneyi. Tionanso zimene Akhristu oyambirira anachita potengera chitsanzo chake. Zifotokozanso chifukwa chake ndi zothandiza masiku ano kukhala pa ubwenzi wabwino ndiponso wolimba, komanso mmene tingachitire zimenezi.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
TSAMBA 12
Mmene Misonkhano Yachigawo Itatu Inasinthira Moyo Wanga
TSAMBA 22
Kodi ‘Mwazika Mizu ndi Kukhazikika pa Maziko’?
TSAMBA 26
Kulambira kwa Pabanja N’kofunika Kwambiri Kuti Tidzapulumuke
TSAMBA 29
Kodi Mwapatula Nthawi Yophunzirira Baibulo?
TSAMBA 32