Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w08 11/15 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Nsanja ya Olonda—2008
  • Timitu
  • NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
  • Cholinga cha Nkhani Zophunzira
  • M’MAGAZINI INO MULINSO:
Nsanja ya Olonda—2008
w08 11/15 tsamba 1-2

Zamkatimu

November 15, 2008

Magazini Yophunzira

NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:

January 5-11, 2009

Thandizani Osochera Kubwerera M’gulu la Nkhosa

TSAMBA 8

NYIMBO ZOIMBA: 47, 101

January 12-18, 2009

Athandizeni Kubwerera Mwamsanga

TSAMBA 12

NYIMBO ZOIMBA: 116, 184

January 19-25, 2009

Samalirani Thanzi Lanu M’njira Yogwirizana ndi Malemba

TSAMBA 23

NYIMBO ZOIMBA: 44, 182

January 26, 2009–February 1, 2009

“Tsutsani Mdyerekezi” Monga Anachitira Yesu

TSAMBA 27

NYIMBO ZOIMBA: 174, 191

Cholinga cha Nkhani Zophunzira

Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 8-16

M’nkhanizi tiphunzira mmene akulu ndiponso anthu ena mumpingo angathandizire abale ndi alongo amene achoka m’gulu la nkhosa la Mulungu. Nkhani zimenezi zikuthandizani kudziwa zimene mungachite kuti muthandize Akhristu ofooka. Zikuthandizaninso kuyankha funso lakuti, kodi anthu amene akubwerera m’gulu ayenera kuyembekezera kudzalandiridwa motani?

Nkhani Yophunzira 3 MASAMBA 23-27

Mwachibadwa anthufe timaganizira za thanzi lathu. N’chifukwa chake Mboni za Yehova zikadwala zimafuna kulandira chithandizo. Komabe m’pofunika ‘kuganiza bwino.’ (Tito 2:12) Ndipotu chofunika kwambiri ndicho kusamalira thanzi lathu lauzimu ndi kulimbitsa ubwenzi wathu ndi Mulungu.

Nkhani Yophunzira 4 MASAMBA 27-31

Dziwani mmene Yesu Khristu anaperekera chitsanzo potsutsa Mdyerekezi. Nkhani imeneyi ikusonyeza kuti Mulungu amamukhulupirira Mwana wake ndipo ikupereka zifukwa zake. Ikusonyeza zimene zinam’thandiza Yesu kuti atsutse Mdyerekezi ndipo ikufotokoza mmene ifenso tingachitire zimenezi.

M’MAGAZINI INO MULINSO:

Kodi Mumafuna Mutakhala Munthu Wotani?

TSAMBA 3

Kutumikira Mulungu ndi “Mtima Umodzi ndi Maganizo Amodzi”

TSAMBA 6

“Titsatire Zinthu Zodzetsa Mtendere”

TSAMBA 17

Mawu a Yehova Ndi Amoyo​—Mfundo Zazikulu za M’makalata a Yakobe ndi Petulo

TSAMBA 20

Mpukutu Wotchedwa “Nyimbo ya Panyanja” Umatithandiza Kudziwa Zinthu Zakale

TSAMBA 32

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena