Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 1992
Zosonyeza deti la kope lopezekamo nkhaniyo
BAIBULO
Chuma Chopezedwa pa Miulu ya Zinyalala ya Igupto (Malembo Apamanja a Oxyrhynchus), 2/15
Kodi Limadzitsutsa? 7/15
Kumasula Yomalizira ya Mipukutu ya ku Nyanja Yakufa, 1/1
Malembo Apamanja Achitsanzo Achihebri, 10/15
Matembenuzidwe a mu Afirika, 9/1
Mphatso Yochokera kwa Mulungu, 5/15
Nkhondo ya Baibulo Lachispanya Yakukhalapobe, 6/15
Phindu la Malembo Apamanja Agumbwa a Nash, 12/15
LIPOTI LA OLENGEZA UFUMU
1/1, 2/1, 3/1, 4/1, 5/1, 6/1, 7/1, 8/1, 9/1, 12/1
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
Akavalo Anyanga Imodzi, 6/1
Kodi Atumwi Anakaikira Pamene Yesu Woukitsidwayo Anawonekera kwa Iwo? (Mat. 28:17), 12/1
Kodi Farao Anakwatira Sara? 2/1
Kodi Mose Anali “Kristuyo”? (Aheb. 11:26), 11/15
‘Kodi Njira ya Mwamuna ndi Namwali’ “njodabwitsa Kwambiri”? (Miy. 30:19, NW), 7/1
Kodi Yesu Anadziŵa kuti Yohane Mbatizi Akayamba Kufa? (Mat. 11:11), 2/15
Kodi Yobu Anali Yekha Wokhulupirika? (Yobu 1:8), 8/1
Kodi Zakariya Anali Wogontha ndi Wosalankhula? (Luka 1:62), 4/1
Kugula Katundu Wakuba, 6/15
Kusunga Masiku Akubadwa, 9/1
Nchifukwa Ninji Nowa Anatumiza Khungubwe Ndiyeno Njiŵa? 1/15
Nsanganizo za Mwazi m’Chakudya, 10/15
Wochititsa Pangano Ayenera Kufa? (Aheb. 9:16), 3/1
MALO A KU DZIKO LOLONJEZEDWA
Anagaŵira Aisrayeli Zosoŵa Zawo m’Sinai, 5/1
Gennesaret—‘Wodabwitsa ndi Wokongola,’ 1/1
Gerasa—Kumene Ayuda ndi Agiriki Anakumana, 7/1
Idyani Chakudya—Idyani Mkate, 9/1
Kupita ku Silo—Ana Abwino ndi Oipa, 11/1
Yenderani Dzikolo, Yenderani Nkhosa! 3/1
MBONI ZA YEHOVA
Amwenye Achigoajiro Alabadira (Colombia, Venezuela), 5/15
Anafika Mosasamala Kanthu za Mavuto ndi Upandu, 7/1
Bukhu Latsopano Lisangalatsa Mamiliyoni (Munthu Wamkulu Koposa), 2/15
Chilengezo (Chithandizo ku Bungwe Lolamulira), 4/15
Chipatala Chotchuka, Nyumba Yaufumu Yapadera (Australia), 8/15
Chowonadi Chisefukira m’Mudzi wa Madzi Ambiri (Lebanon), 10/15
Khoti Lalikulu la Nigeria Lichirikiza Ufulu Wachipembedzo, 12/15
Kulalikira m’Limodzi la Madoko Aakulu Koposa Padziko (Netherlands), 4/15
Kulalikira m’Maputo (Mozambique), 8/15
Kupereka Chidziŵitso mu Namibia, 11/15
Kupeza Chimwemwe Chenicheni mu “Paradaiso” (Hawaii), 9/15
Kusonkhana Ndi Okonda Ufulu Woperekedwa ndi Mulungu, 1/15
Kusonkhanitsa “Zofunika” mu Poland, 7/15
Kututa Olambirawo, 1/1
Kuwafikira “Anthu Amitundu Yonse” m’Belgium, 12/15
Kuŵala Monga Zounikira (Central African Republic), 10/1
“Madzi a Moyo” Atumphuka ku Cape Verde, 3/15
Mboni za Yehova—Gulu la Dzinalo (Vidiyokaseti), 10/1
Omaliza Maphunziro a Gileadi, 6/1, 12/1
Tawonani Zimene Yehova Wachita! (Ethiopia), 11/1
Ulendo Wokapereka Chithandizo ku Ukraine, 3/15
Umphumphu Wachikristu m’Liberia Wokanthidwa ndi Nkhondo, 1/1
Yehova Anatisamalira Pansi pa Chiletso—Gawo 1, 4/15
Yehova Anatisamalira Pansi pa Chiletso—Gawo 2, 5/1
Yehova Anatisamalira Pansi pa Chiletso—Gawo 3, 5/15
Zisumbu za Indian Ocean Zimva Mbiri Yabwino, 2/15
MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU
Akulu—Bwezani Ena Mumzimu Wachifatso, 11/15
Akulu—Gaŵirani Mathayo! 10/15
“Bwererani Kudza kwa Ine, Ndipo Ine Ndidzabwerera kwa inu,” 8/1
Chitonthozo m’Nthaŵi ya Nsautso, 7/15
Khalani ndi Mzimu Wakudzimana! 2/1
Kodi Mwaŵerengera Mtengo? 8/15
‘Kodi Ndiyenera Kubatizidwa?’ 10/1
‘Kudandaulira mwa Chikondi,’ 4/15
Mungathe Kulimbana ndi Kugwiritsidwa Mwala! 9/15
Nchifukwa Ninji Kunama Kuli Kosavuta Choncho? 12/15
Otanganitsidwa m’Ntchito Zakufa Kapena Muutumiki wa Yehova? 7/1
Phunzirani Kumvera Mwakulandira Chilango, 10/1
‘Tavalani Zida Zonse za Mulungu,’ 5/15
Tsatirani Njira Yopambana ya Chikondi, 7/15
NKHANI ZA MOYO WA MUNTHU
Chisangalalo Chimene Kutumikira Yehova Kwandibweretsera (G. Brumley), 12/1
“Kukoma Mtima Kwake Kwachikondi Kwakhaladi Kwamphamvu” (J. Vergara Orozco), 2/1
Kulondola Chonulirapo Choikiridwa Pausinkhu Wazaka Zisanu ndi Chimodzi (S. Cowan), 3/1
Ndinadzichepetsa Ndipo Ndinapeza Chimwemwe (V. Brandolini), 8/1
Ndinalabadira m’Nthaŵi Yakututa (W. Remmie), 7/1
Ndinapeza Chowonadi Nditatuluka m’Ndende ya Buchenwald (R. Séglat), 6/1
Njira ya Mulungu Ndiyo Yabwino Koposa Yokhalira ndi Moyo (E. Kankaanpää), 4/1
Pamene Wina Aitana, Kodi Mumayankha? (S. Tohara), 11/1
Yehova Wandisamalira Bwino (S. Wharerau), 9/1
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRIDWA
Adzapulumuka Ndani “Nthaŵi ya Nsautso”? 5/1
Akristu Onse Owona Ayenera Kukhala Alaliki, 9/1
Akulu, Weruzani Mwachilungamo, 7/1
“Akunga Yehova Mulungu Wathu Ndani?” 11/15
Anthu Aufulu Koma Oŵerengeredwa Thayo, 6/1
Chimwemwe Chosatha Chiyembekezera Opatsa Aumulungu, 1/15
Chimwemwe Chowona Potumikira Yehova, 5/15
Chirimikani mu Ufulu Woperekedwa ndi Mulungu! 3/15
Chitanipo Kanthu Kuti Banja Lanu Likaloŵe m’Dziko Latsopano la Mulungu, 10/15
Chitsanzo Chouziridwa cha Ntchito Yaumishonale Wachikristu, 9/1
Kanani Zoyerekezera Zaudziko, Londolani Zenizeni Zaufumu, 7/15
Khalani Ogalamuka mu “Nthaŵi ya Mapeto,” 5/1
Kodi “Dongosolo Latsopano la Dziko” la Anthu Layandikira? 4/1
Kodi Khoka ndi Nsomba Zimatanthauzanji kwa Inu? 6/15
Kodi Mudzalabadira Chikondi cha Yesu? 2/15
Kodi Mukuthamanga Motani m’Makani a Moyo? 8/1
Kodi Ukwati Ndiwo Mfungulo Yokha ya Chimwemwe? 5/15
Kristu Anada Kusayeruzika—Kodi Mumatero? 7/15
Kuchingamira Dziko Latsopano la Mulungu la Ufulu, 4/1
Kukhalapo kwa Mesiya ndi Ulamuliro Wake, 10/1
Kukonda Yehova Kumasonkhezera Kulambira Kowona, 1/1
Kumbukirani Tsiku la Yehova, 5/1
Kusodza Anthu m’Nyanja ya Dziko Lonse, 6/15
Kutumikira Monga Asodzi a Anthu, 6/15
Kuyenda Ndi Mtima Umodzi, 12/15
‘Lolani Kupita Patsogolo Kwanu Kuwonekera,’ 8/1
Madalitso a Yehova Alemeretsa, 12/1
Makonzedwe a Yehova Achikondi a Ukwati, 10/15
Maphunziro m’Nthaŵi ya m’Baibulo, 11/1
Maphunziro Okhala ndi Cholinga, 11/1
‘M’Dzina la Mzimu Woyera,’ 2/1
Mlungu Umene Unasintha Dziko, 3/1
Mphatso ya Yehova ya Mzimu Woyera, 2/1
“Mubwere Nalo Limodzi Limodzi Lonse la Khumi ku Nyumba Yosungiramo,” 12/1
Munthu Wamkulu Woposa Onse Amene Anakhalapo, 2/15
Musaphonye Chifuno cha Ufulu Woperekedwa ndi Mulungu, 3/15
Mzimu wa Yehova Umatsogolera Anthu Ake, 9/15
Nzika Kapena Mlendo, Mulungu Akulandirani! 4/15
‘Opatsidwa’ Ali Mphatso ya Yehova, 4/15
Pitirizanibe Kumangirirana, 8/15
“Tapeza Ife Mesiya”! 10/1
Tsiku Loyenera Kulikumbukira, 3/1
Tumikirani Yehova Mokhulupirika, 11/15
Ufulu Woperekedwa ndi Mulungu Umabweretsa Chimwemwe, 3/15
Ufulu Wowona—Wochokera ku Magwero Otani? 4/1
Ugwiritsireni Ntchito Mwanzeru Ufulu Wanu Wachikristu, 6/1
Wopani Yehova ndi Kulemekeza Dzina Lake Loyera, 1/1
Yehova Agwiritsira Ntchito “Chopusa” Kupulumutsa Okhulupirirawo, 9/15
Yehova Amakhululukira Koposa, 9/15
Yehova Amakonda Opatsa Mokondwerera, 1/15
Yehova Sayenera Kuimbidwa Mlandu, 11/15
Yehova, Wochita Zinthu Zodabwitsa, 12/15
Yehova, “Woweruza wa Dziko Lonse” Wopanda Tsankho,” 7/1
Zosangulutsa Pocheza—Sangalalani ndi Mapinduwo, Peŵani Misampha, 8/15
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Aneneri Onyenga, 2/1
Chigumula Chosaiŵalika, 1/15
Chigumula m’Nthano Zadziko, 1/15
Chikristu Chadziko ndi Malonda a Akapolo, 9/1
Chimene Ufumu wa Mulungu Umatanthauza, 3/15
Chiyembekezo Chimagonjetsa Kutaya Mtima, 7/1
Diocletian Aukira Chikristu, 6/15
Dipo la Anthu Ambiri, 6/15
Dziko Lopanda Uchimo—Motani? 11/1
Justin—Wanthanthi, Wochirikiza, ndi Wofera Chikhulupiriro, 3/15
Kodi Abambo Autumwi Anaphunzitsa Utatu? 2/1
Kodi Kuchiritsa Kwachikhulupiriro Kumavomerezedwa ndi Mulungu? 6/1
Kodi Kwenikweni Uthenga Wabwino Ndiwo Chiyani? 12/15
Kodi Mafano Angakuyandikitseni ndi Mulungu? 2/15
Kodi Mtundu wa Anthu Ukufunikiradi Mesiya? 10/1
Kodi Muli ndi Chikhulupiriro Chonga cha Eliya? 4/1
Kodi Mulungu Amamvetsera Pamene Mupemphera? 4/15
Kodi Ochirikiza Anaphunzitsa Utatu? 4/1
Kodi Tilambire Mulungu Uti? 1/1
Kodi Uchimo Mumauwona Motani? 11/1
Kodi Uthenga Wabwino Ungakupindulitseni Motani? 12/15
Kubadwanso, 11/15
‘Kulandira Chidziŵitso cha Mulungu ndi Yesu,’ 3/1
Kulankhula m’Malilime, 8/15
Kupembedza Mafano—Nkhani Yamkangano, 2/15
Kuyamikira Mphatso ya Moyo, 8/1
Mavuto a Banja—Chizindikiro cha Nthaŵi, 10/15
Mbadwo wa 1914—Chaka Chimene Chinagwedeza Dziko, 5/1
Mbadwo wa 1914—Nchifukwa Ninji Uli Wapadera? 5/1
Mesiya—Kodi Ndiye Chiyembekezo Chenicheni? 10/1
Mmene Chikhulupiriro Chingathandizire Odwala, 6/1
Moyo—Mphatso Yochokera kwa Mulungu, 8/1
Mtanda—Chizindikiro cha Chikristu? 11/15
Mtundu wa Chisungiko Chimene Mumachikhumba, 3/1
Munthu Wophunzira (Paulo), 11/1
Nchifukwa Ninji Anthu Abwino Amavutika? 9/15
Ndani Ali ndi Chiyanjo cha Mulungu? 12/1
Njira ya Kubwereranso, 8/15
Nkhunda Zoulukira ku Zikwere Zawo, 7/15
Paulo Alimbana ndi Plato Ponena za Chiukiriro, 5/15
Sali Ochita Malonda Nawo Mawu a Mulungu, 12/1
Ubatizo “Mwa Dzina La,” 10/15
Utatu—Pamene ndi Mmene Unayambira? 8/1
Zolinganiza za Chisungiko cha Padziko Lonse, 3/1
Zotuta za Chikristu Chadziko mu Afirika, 9/1
YEHOVA
“Bwererani Kudza kwa Ine, Ndipo Ine Ndidzabwerera kwa inu,” 8/1
Ndimnansi Wanu Kapena Bwenzi Lanu? 6/1
YESU KRISTU
“Umulungu wa Kristu,” 1/15