Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w88 9/15 tsamba 32
  • Chothandizira Kuphunzitsa Chozizwitsa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Chothandizira Kuphunzitsa Chozizwitsa
  • Nsanja ya Olonda—1988
Nsanja ya Olonda—1988
w88 9/15 tsamba 32

Chothandizira Kuphunzitsa Chozizwitsa

MWANA wachichepere angakumbukire zoposa zimene mumalingalira. Mu kalata ya chiyamikiro kaamba ka makaseti tepi a Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo, (Chingelezi) mayi wochokera ku Florida (U.S.A.) akulemba ponena za mwana wake wamwamuna wa zaka zisanu zakubadwa:

“Ngati mumufunsa iye kokha ndi nambala, iye amadziŵa chimene nkhaniyo imanena. Iye sanadziŵebe kuŵerenga koma waloweza nkhanizo ndipo angazinene izo pa mtima. Anthu andiuza ine kuti ana awo sangapite kukagona popanda bulangeti kapena zoseŵeretsa. Wanga sangagone popanda choseŵerera tepi chake chotsegulidwa. Iye amamvetsera ku nkhanizo nthaŵi zonse. Iye amagona usiku uliwonse akumvetsera ku izo. Pano pali chithunzi chake akumvetsera ku izo.”

Kumvetsera ku makaseti a nkhani 116 mu Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo kudzathandiza achichepere anu kuphunzira chimene Baibulo limanena. Kodi mukugwiritsira ntchito chothandizira kuphunzitsa chabwino kwambiri chimenechi? Alubamu yokhala ndi makaseti anayi iri kokha K64; nthaŵi yoseŵerera maora asanu ndi theka.

Chonde tumizani, mutalipiriratu positi, alubamu ya brown vinyl yokhala ndi makaseti tepi anayi a Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo (Chingelezi). Ndatsekeramo K64 (Zambia). (Kunja kwa Zambia, lemberani ofesi ya nthambi ya Watch Tower ya kwanuko kaamba ka mtengo.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena