Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g97 3/8 tsamba 2
  • Tsamba 2

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tsamba 2
  • Galamukani!—1997
  • Timitu
  • Upandu Wolinganiza Mmene Umakukhudzirani 3-10
  • Choonadi Ponena za Bodza 17
  • Kodi Ana Ayenera Kudzisankhira Chipembedzo Chawo? 20
Galamukani!—1997
g97 3/8 tsamba 2

Tsamba 2

Upandu Wolinganiza Mmene Umakukhudzirani 3-10

Upandu wapadziko lonse umakhudza aliyense. Zinthu zonse zakwera mtengo—kuyambira kutaya zinyalala mpaka majuwelo, zovala mpaka simenti. Apandu amaopseza ndi kupseteka oweruza, apolisi, ndi andale. Kodi pali njira youthetsera?

Choonadi Ponena za Bodza 17

Monga momwe chotengera chadothi chingaphwanyikire chitagwetsedwa, unansi wamtengo wapatali nawonso ungawonongeke ndi bodza. Kodi ndi choonadi chanji ponena za bodza chimene tiyenera kudziŵa?

Kodi Ana Ayenera Kudzisankhira Chipembedzo Chawo? 20

Makolo ena amanena kuti ana sayenera kuphunzitsidwa chipembedzo koma kuti ayenera kudzisankhira okha atakula. Kodi Baibulo limanenanji?

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

Mapu: Mountain High Maps® Copyright © 1995 Digital Wisdom, Inc.

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

The Doré Bible Illustrations/Dover Publications, Inc.

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena