Tsamba 2
Ubombo—Kodi Umatikhudza Motani? 3-10
Umbombo wa anthu ukuwononga chuma cha dziko lapansi. Ukudyera masuku pamutu osauka ndi kulemeza achuma. Kodi munga- pulumuke bwanji m’dziko lodzaza umbombo? Kodi umbombo udzathadi?
Kodi Dziko Lapansi Lidzathera m’Moto? 30
Zaka mazana ambiri, zipembedzo zambiri zaphunzitsa kuti dziko lapansi lidzawonongeka ndi moto. Kodi kwenikweni lingaliro la Baibulo nlotani?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Dziko Lapansi pamasamba 2-4, 6, 9, ndi 30: Latengedwa pa chithunzithunzi cha NASA