Tsamba 2
Kodi Mumaŵerengera Agogo? 3-11
Posachedwapa kwakhala chikhoterero cha kunyalanyaza agogo kuwayesa ngati akunja. Kodi mukuchitira agogo motani m’banja mwanu? Kodi muyenera kuwaona motani?
Kodi Mungachitenji ndi Fungo Loipa la m’Kamwa? 12
Fungo loipa la m’kamwa limakhudza aliyense. Pezani chifukwa chake, ndipo dziŵani zimene mungachite nalo.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Life