Tsamba 2
Kodi Chakudya Chanu Chilidi Chomanga Thupi? 3-7
Anthu miyandamiyanda padziko lonse samadya kaŵirikaŵiri chakudya chomangadi thupi. Kadyedwe kosakwanira kamapha. Kodi pali njira zilizonse zothetsera zimenezi?
Kodi Mulungu Amakondwera Kutiona Tikuvutika? 8
Anthu ambiri amakhulupiriradi kuti Mulungu amakondwera kuona okhulupirira akuvutika. Kodi zimenezo nzanzeru? Kodi nzogwirizana ndi Baibulo?