Tsamba 2
Anthu akhala akuyesa maboma kwa zaka mazana ambiri. Komabe, kodi titayesa maboma ameneŵa pamiyeso, timapezanji? Kodi pali chifukwa chirichonse chokhalira achidaliro kuti boma labwinopo likubwera? Kuti tifunefune mayankho odalirika, tiyeni titembenuzire chisamaliro paboma.
[Mawu a Chithunzi patsamba 5]
Cover (Napoleon): Painting after David, Musée national du château de Versailles et de Trianon, France.