Baibo ya Cimasulilo ca Dziko Latsopano Za m’Buku la 2 Timoteyo 2 TIMOTEYO ZA M’BUKULI 1 Mau oyamba (1, 2) Paulo ayamika Mulungu cifukwa ca cikhulupililo ca Timoteyo (3-5) Kukolezela mphatso ya Mulungu ngati moto (6-11) Kugwilitsitsa mau olondola (12-14) Adani komanso mabwenzi a Paulo (15-18) 2 Kuphunzitsa oyenelela kukhala aphunzitsi (1-7) Kupilila mabvuto cifukwa ca uthenga wabwino (8-13) Kufotokoza bwino mau a uthenga wabwino (14-19) Kuthawa zilakolako za unyamata (20-22) Mocitila ndi otsutsa (23-26) 3 Masiku otsiliza adzakhala nthawi yobvuta (1-7) Kutengela citsanzo ca Paulo mosamala (8-13) “Pitiliza kutsatila zimene unaphunzila” (14-17) Malemba onse anauzilidwa ndi Mulungu (16) 4 “Uzikwanilitsa mbali zonse za utumiki wako” (1-5) Lalikila mau modzipeleka (2) “Ndamenya nkhondo yabwino” (6-8) Zina zimene Paulo anakamba (9-18) Kupeleka moni (19-22)