Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa Zamkatimu Njira, Choonadi ndi Moyo GAWO 1 GAWO 1 Zimene Zinachitika Yesu Asanayambe Utumiki Wake MUTU 1 Mauthenga Awiri Ochokera kwa Mulungu MUTU 2 Yesu Analemekezedwa Asanabadwe MUTU 3 Kubadwa kwa Wokonza Njira MUTU 4 Mariya Anakhala ndi Pakati Asanakwatiwe MUTU 5 Kodi Yesu Anabadwa Liti Ndipo Anabadwira Kuti? MUTU 6 Mwana Amene Mulungu Analonjeza MUTU 7 Okhulupirira Nyenyezi Anapita Kukaona Yesu MUTU 8 Anathawa Mfumu Yankhanza MUTU 9 Yesu Anakulira ku Nazareti MUTU 10 Yosefe ndi Banja Lake Anapita ku Yerusalemu MUTU 11 Yohane M’batizi Anakonza Njira GAWO 2 GAWO 2 Mmene Utumiki wa Yesu Unayambira MUTU 12 Zimene Zinachitika Pamene Yesu Ankabatizidwa MUTU 13 Zimene Yesu Anachita Atayesedwa MUTU 14 Yesu Anayamba Kupeza Ophunzira MUTU 15 Chozizwitsa Choyamba Chimene Yesu Anachita MUTU 16 Yesu Anali Wodzipereka pa Kulambira Mulungu MUTU 17 Yesu Anaphunzitsa Nikodemo MUTU 18 Ntchito ya Yesu Inayamba Kuwonjezeka Kuposa ya Yohane MUTU 19 Yesu Analalikira Mayi wa ku Samariya GAWO 3 GAWO 3 Yesu Analalikira Kwambiri ku Galileya MUTU 20 Chozizwitsa Chachiwiri Chimene Yesu Anachita ku Kana MUTU 21 Zimene Zinachitika Yesu Ali ku Sunagoge wa ku Nazareti MUTU 22 Yesu Anaitana Ophunzira Ake 4 MUTU 23 Yesu Anachita Zozizwitsa Ali ku Kaperenao MUTU 24 Yesu Analalikira M’madera Ambiri a ku Galileya MUTU 25 Yesu Anachitira Chifundo Munthu Wakhate N’kumuchiritsa MUTU 26 “Machimo Ako Akhululukidwa” MUTU 27 Yesu Anaitana Mateyu MUTU 28 N’chifukwa Chiyani Ophunzira a Yesu Sankasala Kudya? MUTU 29 Kodi Kunali Kulakwa Kugwira Ntchito Yabwino pa Sabata? MUTU 30 Kodi Pali Ubale Wotani Pakati pa Yesu ndi Mulungu? MUTU 31 Anabudula Ngala za Tirigu pa Tsiku la Sabata MUTU 32 Kodi Malamulo Ankalola Munthu Kuchita Chiyani pa Sabata? MUTU 33 Ulosi wa Yesaya Unakwaniritsidwa MUTU 34 Yesu Anasankha Atumwi 12 MUTU 35 Ulaliki Wotchuka wa Paphiri MUTU 36 Kapitawo wa Asilikali Anasonyeza Kuti Anali ndi Chikhulupiriro MUTU 37 Yesu Anaukitsa Mwana Wamwamuna wa Mzimayi Wamasiye MUTU 38 Yohane Yemwe Anali M’ndende Ankafuna Kumva Kuchokera kwa Yesu MUTU 39 Tsoka kwa M’badwo Umene Sunamvere MUTU 40 Anawaphunzitsa Kukhululukira Ena MUTU 41 Kodi Yesu Ankazitenga Kuti Mphamvu Zochitira Zozizwitsa? MUTU 42 Yesu Anadzudzula Afarisi MUTU 43 Mafanizo Ofotokoza za Ufumu MUTU 44 Yesu Analetsa Mphepo Yamphamvu Panyanja MUTU 45 Anatulutsa Ziwanda Zambiri MUTU 46 Anachira Atagwira Malaya a Yesu MUTU 47 Kamtsikana Kanakhalanso ndi Moyo MUTU 48 Yesu Anachita Zozizwitsa Koma Anakanidwa Ngakhale Kwawo ku Nazareti MUTU 49 Analalikira ku Galileya Komanso Anaphunzitsa Atumwi MUTU 50 Anawakonzekeretsa Kuti Azilalikira Ngakhale Pamene Akuzunzidwa MUTU 51 Anaphedwa pa Tsiku Lokondwerera Kubadwa MUTU 52 Anadyetsa Anthu Masauzande Ambiri ndi Mikate Komanso Nsomba Zochepa MUTU 53 Wolamulira Amene Akhoza Kulamulira Mphepo Yamphamvu MUTU 54 Yesu Ndiye “Chakudya Chopatsa Moyo” MUTU 55 Kudya Mnofu wa Yesu ndi Kumwa Magazi Ake MUTU 56 Kodi Chimaipitsa Munthu N’chiyani? MUTU 57 Yesu Anachiritsa Mtsikana Komanso Munthu Wogontha MUTU 58 Anachulukitsa Mikate Komanso Anachenjeza Ophunzira Ake za Zofufumitsa MUTU 59 Kodi Mwana wa Munthu Ndi Ndani? MUTU 60 Anaona Ulemelero wa Khristu Atasandulika MUTU 61 Yesu Anachiritsa Mnyamata Amene Anali ndi Chiwanda MUTU 62 Kufunika Kokhala Wodzichepetsa MUTU 63 Yesu Anafotokoza Zoyenera Kuchita Anthu Akakhumudwitsana Komanso Ngati Wina Wachita Tchimo MUTU 64 Anawaphunzitsa Kufunika Kokhululukira Ena MUTU 65 Yesu Anaphunzitsa Anthu Ena Ali pa Ulendo Wopita ku Yerusalemu GAWO 4 GAWO 4 Yesu Anakalalikira ku Yudeya MUTU 66 Zimene Zinachitika Yesu Atapita ku Chikondwerero cha Misasa ku Yerusalemu MUTU 67 “Palibe Munthu Amene Analankhulapo Ngati Iyeyo” MUTU 68 Mwana wa Mulungu Ndiye “Kuwala kwa Dziko” MUTU 69 Kodi Atate Wawo Anali Abulahamu Kapena Mdyerekezi? MUTU 70 Yesu Anachiritsa Munthu Amene Anabadwa Wosaona MUTU 71 Afarisi Anatsutsana ndi Munthu Amene Anali Wakhungu MUTU 72 Yesu Anatumiza Ophunzira 70 Kuti Akalalikire MUTU 73 Nkhani ya Msamariya Imatithandiza Kudziwa Mnzathu Weniweni MUTU 74 Zimene Tikuphunzira pa Nkhani Yochereza Alendo Komanso ya Pemphero MUTU 75 Yesu Ananena Zimene Zimachititsa Munthu Kukhala Wodala MUTU 76 Anakadya Kunyumba kwa Mfarisi MUTU 77 Yesu Anapereka Malangizo pa Nkhani ya Chuma MUTU 78 Woyang’anira Nyumba Wokhulupirika Ayenera Kukhala Wokonzeka MUTU 79 Ayuda Ankayembekezera Kuwonongedwa MUTU 80 M’busa Wabwino Komanso Makola Awiri a Nkhosa MUTU 81 Yesu si Mulungu Koma Iye ndi Atate Wake Ndi Amodzi GAWO 5 GAWO 5 Yesu Analalikira Kum’mawa kwa Yorodano Chakumapeto kwa Utumiki Wake MUTU 82 Zimene Zinachitika Pamene Yesu Ankalalikira ku Pereya MUTU 83 Kuitanira Anthu ku Chakudya MUTU 84 Kukhala Wophunzira wa Yesu Ndi Udindo Waukulu MUTU 85 Pamakhala Chisangalalo Munthu Wochimwa Akalapa MUTU 86 Mwana Wotayika Anabwerera MUTU 87 Muzichita Zinthu Mwanzeru Pokonzekera Zakutsogolo MUTU 88 Mmene Zinthu Zinasinthira kwa Munthu Wachuma Komanso kwa Lazaro MUTU 89 Anaphunzitsa ku Pereya Ali pa Ulendo Wopita ku Yudeya MUTU 90 Yesu Ndi “Kuuka ndi Moyo” MUTU 91 Yesu Anaukitsa Lazaro MUTU 92 Pa Anthu 10 Akhate, Mmodzi Anathokoza Yesu MUTU 93 Mwana wa Munthu Adzaonekera MUTU 94 Kupemphera Komanso Kudzichepetsa Ndi Zinthu Ziwiri Zofunika Kwambiri MUTU 95 Anawafotokozera Chifukwa Chothetsera Banja Komanso Kuti Azikonda Ana MUTU 96 Yesu Anayankha Wolamulira Wachinyamata Amene Anali Wolemera MUTU 97 Fanizo la Anthu Ogwira Ntchito M’munda wa Mpesa MUTU 98 Atumwi Anasonyezanso Kuti Ankafuna Udindo Wapamwamba MUTU 99 Yesu Anachiritsa Anthu Akhungu Komanso Anathandiza Zakeyu MUTU 100 Fanizo la Ndalama 10 za Mina GAWO 6 GAWO 6 Zimene Yesu Anachita Kumapeto kwa Utumiki Wake MUTU 101 Yesu Anakadya Chakudya ku Nyumba kwa Simoni ku Betaniya MUTU 102 Mfumu Inalowa mu Yerusalemu Itakwera pa Bulu MUTU 103 Yesu Anayeretsanso Kachisi MUTU 104 Kodi Ayuda Anakhulupirira Yesu Atamva Mulungu Akulankhula? MUTU 105 Yesu Anagwiritsa Ntchito Mtengo wa Mkuyu Pophunzitsa Anthu za Chikhulupiriro MUTU 106 Mafanizo Awiri Onena za Munda wa Mpesa MUTU 107 Mfumu Inaitanira Anthu ku Phwando la Ukwati MUTU 108 Yesu Analepheretsa Afarisi Kuti Amugwire MUTU 109 Anadzudzula Atsogoleri Achipembedzo Omwe Ankamutsutsa MUTU 110 Tsiku Lomaliza Limene Yesu Anapezeka pa Kachisi MUTU 111 Atumwi Anapempha Chizindikiro MUTU 112 Fanizo la Anamwali Limatiphunzitsa Kufunika Kokhala Tcheru MUTU 113 Fanizo la Matalente Limatiphunzitsa Kufunika Kochita Zinthu Mwakhama MUTU 114 Khristu Akadzayamba Kulamulira Adzaweruza Nkhosa ndi Mbuzi MUTU 115 Yesu Anachita Mwambo Womaliza wa Pasika MUTU 116 Anawaphunzitsa Kudzichepetsa pa Pasika Womaliza MUTU 117 Chakudya Chamadzulo Cha Ambuye MUTU 118 Anakangananso Kuti Wamkulu Ndani MUTU 119 Yesu Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo MUTU 120 Anali Ngati Nthambi Zobala Zipatso Komanso Anali Mabwenzi a Yesu MUTU 121 “Limbani Mtima Ndaligonjetsa Dziko” MUTU 122 Pemphero Lomaliza la Yesu Ali M’chipinda Chapamwamba MUTU 123 Anapemphera Pamene Anali ndi Chisoni Kwambiri MUTU 124 Khristu Anaperekedwa Kenako Anamangidwa MUTU 125 Atamugwira Anapita Naye kwa Anasi Kenako kwa Kayafa MUTU 126 Petulo Anakana Yesu Kunyumba kwa Kayafa MUTU 127 Khoti la Sanihedirini Linaweruza Mlandu wa Yesu Kenako Anapita Naye kwa Pilato MUTU 128 Pilato Komanso Herode Sanamupeze Yesu ndi Mlandu MUTU 129 Pilato Ananena Kuti: “Taonani! Mwamuna Uja ndi Uyu!” MUTU 130 Pilato Anapereka Yesu Ndipo Anthu Anamutenga Kuti Akamuphe MUTU 131 Mfumu Yosalakwa Inavutika Itapachikidwa Pamtengo MUTU 132 “Ndithudi munthu uyu Analidi Mwana wa Mulungu” MUTU 133 Anakonza Thupi la Yesu ndi Kukaliika M’manda MUTU 134 M’manda a Yesu Munalibe Kanthu Chifukwa Anali Ataukitsidwa MUTU 135 Yesu Ataukitsidwa Anaonekera kwa Anthu Ambiri MUTU 136 Anaonekera M’mbali Mwanyanja ya Galileya MUTU 137 Anaonekera kwa Anthu Ambiri Mwambo wa Pentekosite Usanachitike MUTU 138 Khristu Anakhala Kudzanja Lamanja la Mulungu MUTU 139 Yesu Adzabweretsa Paradaiso Kenako Adzamaliza Kugwira Ntchito Imene Anapatsidwa Kuti Mutsanzire Yesu Muyenera . . . Kalozera wa Malemba Kalozera wa Mafanizo Maulosi Ena Onena za Mesiya Malo Amene Yesu Anakhalako Komanso Kuphunzitsa