Mawu a M'munsi
e MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: M’bale akusonyeza kuti amatsanzira chitsanzo cha Yesu posonyeza kuti amaganizira alongo okhulupirika, m’bale akuthandiza alongo awiri kusintha tayala la galimoto yawo, m’bale wina wapita kukaona mlongo wachikulire, ndipo m’bale winanso wapita ndi mkazi wake kunyumba ya mlongo wina ndi mwana wake kuti akachite kulambira kwa pabanja.