Mawu a M'munsi
c Buku lina limati: “Ophunzira ankakhala pamapazi a aphunzitsi awo. Iwo ankachita zimenezi pokonzekera kudzakhalanso aphunzitsi, koma akazi sankaloledwa kukhala aphunzitsi. . . . Choncho amuna ambiri a Chiyuda akanadabwa kwambiri kuona Mariya atakhala pamapazi a Yesu n’kumamumvetsera mwachidwi.”