Mawu a M'munsi
a Alongo athu amakumana ndi mavuto ambiri. Munkhaniyi tiona mmene tingalimbikitsire alongo athuwa potsanzira Yesu. Tionanso kuti Yesu ankapeza nthawi yocheza ndi akazi, kuwayamikira komanso kuwateteza.