Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Anthu ofufuza zinthu zakale anapeza zokolola zambiri zimene zinakwiririka pamalo amene panali mzinda wa Yeriko ndipo izi zikusonyeza kuti mzindawu sunazunguliridwe ndi Aisiraeli kwa nthawi yaitali moti chakudya sichinathe mumzindawo. Popeza Aisiraeli sanaloledwe kulanda zinthu mumzinda wa Yeriko, nthawi imene anagonjetsa mzindawu inali yabwino chifukwa m’minda munali chakudya chambirimbiri.​—Yos. 5:10-12.

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena