Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Yosefe anatchulidwa komaliza pamene Yesu anali ndi zaka 12. Pa nthawi imene Yesu anachita chinthu chodabwitsa choyamba, chomwe ndi kusandutsa madzi kukhala vinyo, Yosefe sanatchulidwe ndipo satchulidwanso munkhani zina zotsatira. Ndipo Yesu ali pamtengo wozunzikirapo, anauza mtumwi Yohane kuti azisamalira mayi ake. Akanakhala kuti Yosefe anali moyo, Yesu sakananena zimenezi.​—Yoh. 19:26, 27.

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena