Mawu a M'munsi
d Buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? lathandiza anthu ambiri kuphunzira Baibulo motsatira nkhani imodzi m’chaputala chilichonse cha m’bukuli. Mwachitsanzo, Chaputala 17 chimafotokoza zimene Malemba amanena pa nkhani ya pemphero.