Mawu a M'munsi
b Zikuoneka kuti mzinda wa Samariya, womwe unali likulu la dziko la Isiraeli, unali ndi anthu 20,000 kapena 30,000 m’nthawi ya Yona. Chiwerengerochi chinali chochepa kwambiri pafupifupi nthawi zisanu kuyerekeza ndi chiwerengero cha anthu a ku Nineve. Panthawi imene mzinda wa Nineve unali wotukuka kwambiri, uyenera kuti unali waukulu kwambiri padziko lonse.