Mawu a M'munsi
a M’mavesi a m’Baibulo amene tawatchula ndi kuwagwira mawu m’ndime ino ndi m’ndime yotsatira, liwu la m’chinenero choyambirira limene alimasulira kuti “chifundo” ndi “kukoma mtima.” M’Baibulo la New World Translation analimasulira moyenera kuti “kukoma mtima kwachikondi.”