Mawu a M'munsi
a Liwu la Chigiriki limene Paulo analigwiritsa ntchito limene lamasuliridwa kuti “utsiru” ndi limenenso analigwiritsa ntchito m’Baibulo la Septuagint ya Chigiriki pomasulira mawu amene Solomo anawagwiritsa ntchito mobwerezabwereza m’buku la Mlaliki, monga pa mawu akuti ‘zonse ndi chabe.’—Mlaliki 1:2, 14; 2:11, 17; 3:19; 12:8.