Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Chiŵerengero chenicheni cha asilikali ndi anthu wamba omwe afa sichikudziŵika. Mwachitsanzo, buku la 1998 lakuti Facts About the American Wars (Zoona Zake za Nkhondo za America) linanenapo za nkhondo yachiŵiri yokha yadziko lonse kuti: “Mabuku ambiri amapereka chiwonkhetso cha omwe anafa pa nkhondo yachiŵiri ya padziko lonse (asilikali ndi anthu wamba) kukhala 50 miliyoni koma ambiri omwe afufuza mosamalitsa nkhaniyi akukhulupirira kuti chiŵerengero cholondola n’chokwera kwambiri, ngakhale kuŵirikiza kaŵiri nambala imeneyo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena