Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Zina za nyimbo zaposachedwapa zingakhale zovutirapo pang’ono kwa ife kuziimba choyamba, koma pambuyo pa kuzoloŵerana nazo, izo zingatsimikizire kukhala zokondedwa zathu za pamtima. Mwachitsanzo, pamene bukhu la nyimbo lapapitapo linabwera, nyimbo 88, “Kuyenda mu Umphumphu,” siinakondedwe mu dziko lina, koma pambuyo pake iyo inakhala nyimbo yokondedwa kwambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2026 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena